Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 12:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Tsopano Yehova anauza Abulamu kuti: “Tuluka m’dziko lako, pakati pa abale ako, ndi kusiya nyumba ya bambo ako. Upite kudziko limene ndidzakusonyeza.+

  • Genesis 15:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Abulamu atamva zimenezi anati: “Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, mudzandipatsa chiyani ine? Taonani ndilibe mwana ndipo amene adzakhale wolowa nyumba yanga ndi munthu wa ku Damasiko, Eliezere.”+

  • Nehemiya 9:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Inu ndinu Yehova Mulungu woona, amene munasankha Abulamu+ ndi kum’tulutsa ku Uri wa Akasidi+ ndipo munamutcha dzina lakuti Abulahamu.+

  • Ezekieli 33:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 “Iwe mwana wa munthu, anthu okhala m’malo owonongedwa+ akulankhula za dziko la Isiraeli kuti, ‘Abulahamu anali munthu mmodzi koma anatenga dzikoli.+ Ife tilipo ambiri, choncho dzikoli laperekedwa kwa ife kuti likhale lathu.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena