Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Maliko 9:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Iye anawayankha kuti: “Eliya adzabweradi choyamba ndi kubwezeretsa zinthu zonse.+ Koma n’chifukwa chiyani malemba amanena za Mwana wa munthu, kuti ayenera kukumana ndi mavuto ambiri,+ ndi kumuchita zinthu ngati munthu wopanda pake?+

  • Yohane 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Iye anali m’dziko,+ ndipo dziko linakhalapo kudzera mwa iye.+ Koma dzikolo silinamudziwe.

  • Yohane 18:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Pamenepo iwo anafuulanso kuti: “Ameneyo ayi, koma Baraba!” Koma Baraba ameneyu anali wachifwamba.+

  • Yohane 19:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pamenepo Yesu anatulukira panja, atavala chisoti chachifumu chaminga chija ndi malaya akunja ofiirira. Ndipo Pilato anati: “Taonani! Mwamuna uja ndi uyu!”

  • 1 Petulo 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pamene mukubwera kwa iye, amene ndiye mwala wamoyo+ umene anthu+ anaukana,+ koma umene Mulungu anausankha, umenenso uli wamtengo wapatali kwa iye,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena