Chivumbulutso 21:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Maziko+ a mpanda wa mzindawo anawakongoletsa ndi miyala yamtengo wapatali ya mitundu yonse:+ maziko oyamba anali amwala wa yasipi,+ achiwiri wa safiro,+ achitatu wa kalikedo, achinayi wa emarodi,+
19 Maziko+ a mpanda wa mzindawo anawakongoletsa ndi miyala yamtengo wapatali ya mitundu yonse:+ maziko oyamba anali amwala wa yasipi,+ achiwiri wa safiro,+ achitatu wa kalikedo, achinayi wa emarodi,+