Salimo 36:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Amadya ndi kukhuta chakudya chonona m’nyumba mwanu.+Ndipo mumawamwetsa mumtsinje wa zosangalatsa zanu zambiri.+ Salimo 63:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Moyo wanga wakhutira ndi gawo labwino kwambiri, wakhutira ndi zinthu zabwino kwambiri,+Ndipo milomo yanga ikukutamandani ndi mfuu yachisangalalo.+ Mateyu 22:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako inatumanso akapolo ena+ kuti, ‘Kauzeni oitanidwawo kuti: “Ine ndakonza chakudya chamasana,+ ng’ombe zanga komanso nyama zanga zonenepa zaphedwa, ndipo zinthu zonse zakonzedwa kale. Bwerani ku phwando laukwati.”’+
8 Amadya ndi kukhuta chakudya chonona m’nyumba mwanu.+Ndipo mumawamwetsa mumtsinje wa zosangalatsa zanu zambiri.+
5 Moyo wanga wakhutira ndi gawo labwino kwambiri, wakhutira ndi zinthu zabwino kwambiri,+Ndipo milomo yanga ikukutamandani ndi mfuu yachisangalalo.+
4 Kenako inatumanso akapolo ena+ kuti, ‘Kauzeni oitanidwawo kuti: “Ine ndakonza chakudya chamasana,+ ng’ombe zanga komanso nyama zanga zonenepa zaphedwa, ndipo zinthu zonse zakonzedwa kale. Bwerani ku phwando laukwati.”’+