Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 23:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Kodi si mmene nyumba yanga ilili kwa Mulungu?+

      Chifukwa chakuti anachita nane pangano lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale,+

      Analikonza bwino ndipo n’lotetezeka.+

      Chifukwa ndilo chipulumutso changa+ ndi chondikondweretsa,

      Kodi chimenechi sindicho chifukwa chake adzakulitsa panganoli?+

  • Yesaya 61:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Pakuti ine Yehova ndimakonda chilungamo.+ Ndimadana ndi zauchifwamba ndi kupanda chilungamo.+ Ndidzawapatsa malipiro awo mokhulupirika,+ ndipo ndidzachita nawo pangano lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale.+

  • Aheberi 13:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Tsopano, Mulungu wamtendere,+ amene anaukitsa kwa akufa+ m’busa wamkulu+ wa nkhosa+ wokhala ndi magazi a pangano losatha,+ Ambuye wathu Yesu,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena