Deuteronomo 32:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+Njira zake zonse ndi zolungama.+Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita chosalungama.+Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+ Salimo 33:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye amakonda chilungamo ndi chiweruzo chosakondera.+Dziko lapansi ladzaza ndi kukoma mtima kosatha kwa Yehova.+ Salimo 37:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pakuti Yehova amakonda chilungamo,+Ndipo sadzasiya anthu ake okhulupirika.+ ע [ʽAʹyin]Adzawateteza mpaka kalekale.+Koma ana a anthu oipa adzaphedwa.+
4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+Njira zake zonse ndi zolungama.+Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita chosalungama.+Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+
5 Iye amakonda chilungamo ndi chiweruzo chosakondera.+Dziko lapansi ladzaza ndi kukoma mtima kosatha kwa Yehova.+
28 Pakuti Yehova amakonda chilungamo,+Ndipo sadzasiya anthu ake okhulupirika.+ ע [ʽAʹyin]Adzawateteza mpaka kalekale.+Koma ana a anthu oipa adzaphedwa.+