Deuteronomo 32:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anapitiriza kumuyendetsa pamapiri a dziko lapansi,+Moti anadya zokolola za m’minda.+Anapitirizanso kumudyetsa uchi wochokera m’thanthwe,+Ndi mafuta ochokera m’mwala wa nsangalabwi.+ Yesaya 33:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iye ndi amene adzakhale pamalo apamwamba.+ Malo ake okhala adzakhala otetezeka m’matanthwe movuta kufikamo.+ Iye adzapatsidwa chakudya+ ndipo madzi ake sadzatha.”+ Habakuku 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ndiye mphamvu yanga.+ Iye adzachititsa miyendo yanga kukhala ngati ya mbawala,+ moti adzandiyendetsa pamalo anga okwezeka.”+Kwa wotsogolera nyimbo zoimbidwa ndi zipangizo zanga za zingwe.
13 Anapitiriza kumuyendetsa pamapiri a dziko lapansi,+Moti anadya zokolola za m’minda.+Anapitirizanso kumudyetsa uchi wochokera m’thanthwe,+Ndi mafuta ochokera m’mwala wa nsangalabwi.+ Yesaya 33:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iye ndi amene adzakhale pamalo apamwamba.+ Malo ake okhala adzakhala otetezeka m’matanthwe movuta kufikamo.+ Iye adzapatsidwa chakudya+ ndipo madzi ake sadzatha.”+ Habakuku 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ndiye mphamvu yanga.+ Iye adzachititsa miyendo yanga kukhala ngati ya mbawala,+ moti adzandiyendetsa pamalo anga okwezeka.”+Kwa wotsogolera nyimbo zoimbidwa ndi zipangizo zanga za zingwe.
16 Iye ndi amene adzakhale pamalo apamwamba.+ Malo ake okhala adzakhala otetezeka m’matanthwe movuta kufikamo.+ Iye adzapatsidwa chakudya+ ndipo madzi ake sadzatha.”+
19 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ndiye mphamvu yanga.+ Iye adzachititsa miyendo yanga kukhala ngati ya mbawala,+ moti adzandiyendetsa pamalo anga okwezeka.”+Kwa wotsogolera nyimbo zoimbidwa ndi zipangizo zanga za zingwe.