Yobu 42:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano Yehova anathetsa masautso a Yobu+ pamene iye anapempherera anzake aja.+ Kuwonjezera pamenepo Yehova anayamba kum’patsa Yobu zonse zimene anali nazo, kuwirikiza kawiri.+
10 Tsopano Yehova anathetsa masautso a Yobu+ pamene iye anapempherera anzake aja.+ Kuwonjezera pamenepo Yehova anayamba kum’patsa Yobu zonse zimene anali nazo, kuwirikiza kawiri.+