Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 32:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ine ndine wosayenerera kukoma mtima kosatha ndi kukhulupirika konseku, kumene mwandionetsa ine mtumiki wanu.+ Ndinawoloka Yorodano ndilibe kanthu, koma ndodo yokha, ndipo tsopano ndili ndi magulu awiriwa.+

  • 1 Samueli 2:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Yehova ndi Wopereka Umphawi+ ndi Wolemeretsa,+

      Wotsitsa ndiponso Wokweza,+

  • 2 Mbiri 25:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pamenepo Amaziya+ anafunsa munthu wa Mulungu woonayo kuti: “Nanga bwanji za matalente 100 amene ndapereka kwa asilikali a ku Isiraeli aja?”+ Munthu wa Mulungu woonayo anayankha kuti: “Yehova akhoza kukupatsani zambiri kuposa pamenepa.”+

  • Miyambo 22:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Zotsatirapo za kudzichepetsa ndiponso kuopa Yehova ndizo chuma, ulemerero, ndi moyo.+

  • Yesaya 61:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 M’malo mwa manyazi, mudzalandira zinthu zochuluka kuwirikiza kawiri,+ ndipo m’malo mochita manyazi, anthu anga adzafuula ndi chisangalalo chifukwa cha gawo lawo.+ Iwo adzakhala ndi gawo lowirikiza kawiri m’dziko lawo,+ ndipo adzasangalala mpaka kalekale.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena