Ezekieli 39:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “‘Ndidzasonyeza ulemerero wanga pakati pa mitundu ya anthu. Mitundu yonse ya anthu idzaona chiweruzo chimene ndidzapereke+ ndiponso mphamvu za dzanja langa.+
21 “‘Ndidzasonyeza ulemerero wanga pakati pa mitundu ya anthu. Mitundu yonse ya anthu idzaona chiweruzo chimene ndidzapereke+ ndiponso mphamvu za dzanja langa.+