Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 27:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Yehova ndiye kuwala+ kwanga ndi chipulumutso changa.+

      Ndingaopenso ndani?+

      Yehova ndiye malo a chitetezo cha moyo wanga.+

      Ndingachitenso mantha ndi ndani?+

  • Salimo 84:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pakuti Yehova Mulungu ndi dzuwa+ ndiponso chishango.+

      Iye amatikomera mtima ndi kutipatsa ulemerero.+

      Yehova samana anthu oyenda mosalakwa chinthu chilichonse chabwino.+

  • Yesaya 31:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Thanthwe lake lidzachoka chifukwa cha mantha ndipo akalonga ake adzachita mantha chifukwa cha chizindikiro,”+ akutero Yehova, amene kuwala kwake kuli mu Ziyoni ndiponso amene ng’anjo+ yake ili mu Yerusalemu.

  • Yesaya 60:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Dzuwa silidzakhalanso lokuunikira masana, ndipo mwezi sudzakuunikiranso. Kwa iwe, Yehova adzakhala kuwala kosatha mpaka kalekale,+ ndipo Mulungu wako adzakhala kukongola kwako.+

  • Chivumbulutso 22:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Komanso, usiku sudzakhalakonso.+ Sadzafunikiranso kuwala kwa nyale kapena kwa dzuwa, chifukwa Yehova Mulungu adzawaunikira.+ Ndipo adzalamulira monga mafumu kwamuyaya.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena