Yeremiya 43:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamapeto pake anafika ku Iguputo+ chifukwa sanamvere mawu a Yehova ndipo patapita nthawi anakafika ku Tahapanesi.+ Yohane 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Sindikupempha kuti muwachotse m’dziko, koma kuti muwayang’anire kuopera woipayo.+ Chivumbulutso 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mitembo yawo idzagona pamsewu waukulu mumzinda waukulu, umene mophiphiritsira ukutchedwa Sodomu+ ndi Iguputo, kumenenso Ambuye wawo anapachikidwa.+
7 Pamapeto pake anafika ku Iguputo+ chifukwa sanamvere mawu a Yehova ndipo patapita nthawi anakafika ku Tahapanesi.+
8 Mitembo yawo idzagona pamsewu waukulu mumzinda waukulu, umene mophiphiritsira ukutchedwa Sodomu+ ndi Iguputo, kumenenso Ambuye wawo anapachikidwa.+