Salimo 67:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Dziko lapansi lidzapereka zipatso zake.+Mulungu, ndithu Mulungu wathu, adzatidalitsa.+ Salimo 115:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova watikumbukira, ndipo adzapereka madalitso,+Adzadalitsa nyumba ya Isiraeli,+Adzadalitsa nyumba ya Aroni.+ Yesaya 61:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ana awo adzadziwika pakati pa mitundu ya anthu,+ ndipo mbadwa zawo zidzadziwika pakati pa anthu osiyanasiyana. Onse owaona adzazindikira+ kuti iwo ndi ana odalitsidwa ndi Yehova.”+ Yesaya 65:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova wanena kuti: “Monga momwe vinyo watsopano+ amapezekera m’tsango la mphesa ndipo wina amanena kuti, ‘Musaliwononge,+ pakuti muli dalitso mmenemu,’+ inenso ndidzachita zomwezo chifukwa cha atumiki anga, kuti ndisawawononge onse.+
12 Yehova watikumbukira, ndipo adzapereka madalitso,+Adzadalitsa nyumba ya Isiraeli,+Adzadalitsa nyumba ya Aroni.+
9 Ana awo adzadziwika pakati pa mitundu ya anthu,+ ndipo mbadwa zawo zidzadziwika pakati pa anthu osiyanasiyana. Onse owaona adzazindikira+ kuti iwo ndi ana odalitsidwa ndi Yehova.”+
8 Yehova wanena kuti: “Monga momwe vinyo watsopano+ amapezekera m’tsango la mphesa ndipo wina amanena kuti, ‘Musaliwononge,+ pakuti muli dalitso mmenemu,’+ inenso ndidzachita zomwezo chifukwa cha atumiki anga, kuti ndisawawononge onse.+