Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 23:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Mkwiyo wa Yehova sudzatha kufikira atachita zofuna za mtima wake+ ndi kuzikwaniritsa.+ M’masiku otsiriza, anthu inu mudzalingalira zimenezi ndipo mudzazimvetsa.+

  • Yeremiya 30:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Mkwiyo woyaka moto wa Yehova sudzatha kufikira atachita zofuna za mtima wake ndi kuzikwaniritsa.+ M’masiku otsiriza, anthu inu mudzalingalira zimenezi.+

  • Ezekieli 38:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndithu iwe udzabwera ngati mitambo kudzaphimba dzikolo ndi kudzaukira anthu anga Aisiraeli.+ Zimenezi zidzachitika m’masiku otsiriza, ndipo ine ndidzakubweretsa kuti uukire dziko langa.+ Ndidzachita izi kuti anthu a mitundu ina adzandidziwe pamene ndidzadziyeretse pamaso pawo, kudzera mwa iwe Gogi.”’+

  • Danieli 12:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Iye anandiyankha kuti: “Pita Danieli, pakuti mawuwa asungidwa mwachinsinsi ndipo atsekedwa ndi kumatidwa kufikira nthawi yamapeto.+

  • Machitidwe 2:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 ‘“Ndipo m’masiku otsiriza,” akutero Mulungu, “ndidzatsanulira mbali ya mzimu wanga+ pa anthu osiyanasiyana, ndipo ana anu aamuna ndi ana anu aakazi adzanenera. Anyamata anu adzaona masomphenya, ndipo amuna achikulire adzalota maloto.+

  • 2 Timoteyo 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Koma dziwa kuti, masiku otsiriza+ adzakhala nthawi yapadera komanso yovuta.+

  • Chivumbulutso 12:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pa chifukwa chimenechi, kondwerani kumwamba inu ndi inu okhala kumeneko!+ Tsoka+ dziko lapansi ndi nyanja,+ chifukwa Mdyerekezi watsikira kwa inu, ndipo ali ndi mkwiyo waukulu podziwa kuti wangotsala ndi kanthawi kochepa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena