Danieli 8:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Zinthu zimene waziona ndiponso zimene zanenedwa zokhudza madzulo ndi m’mawa, n’zoona.+ Koma iweyo usunge chinsinsi cha masomphenyawo, chifukwa ndi okhudza masiku am’tsogolo.”+ Danieli 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Koma iwe Danieli, sunga mawuwa mwachinsinsi ndipo utseke ndi kumata bukuli+ kufikira nthawi yamapeto.+ Anthu ambiri adzayenda uku ndi uku ndipo adzadziwa zinthu zambiri zoona.”+
26 “Zinthu zimene waziona ndiponso zimene zanenedwa zokhudza madzulo ndi m’mawa, n’zoona.+ Koma iweyo usunge chinsinsi cha masomphenyawo, chifukwa ndi okhudza masiku am’tsogolo.”+
4 “Koma iwe Danieli, sunga mawuwa mwachinsinsi ndipo utseke ndi kumata bukuli+ kufikira nthawi yamapeto.+ Anthu ambiri adzayenda uku ndi uku ndipo adzadziwa zinthu zambiri zoona.”+