Miyambo 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 kuti alandire malangizo+ amene amathandiza munthu kuzindikira,+ kuchita zolondola,+ zachilungamo+ ndi zowongoka.+ Miyambo 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa nthawiyo udzanena kuti: “Ndinkadana ndi malangizo* ine,+ ndipo mtima wanga sunkavomereza kudzudzula.+ Zefaniya 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno ndinati, ‘Mosakayikira udzandiopa ndipo udzalola kulangizidwa’+ kuti malo ake okhala asawonongedwe,+ pakuti ndidzamuimba mlandu wa zonsezi.+ Koma zinthu zawo zonse zimene anali kuchita zinali zowawonongetsa ndipo anazichitadi mofulumira.+
3 kuti alandire malangizo+ amene amathandiza munthu kuzindikira,+ kuchita zolondola,+ zachilungamo+ ndi zowongoka.+
12 Pa nthawiyo udzanena kuti: “Ndinkadana ndi malangizo* ine,+ ndipo mtima wanga sunkavomereza kudzudzula.+
7 Ndiyeno ndinati, ‘Mosakayikira udzandiopa ndipo udzalola kulangizidwa’+ kuti malo ake okhala asawonongedwe,+ pakuti ndidzamuimba mlandu wa zonsezi.+ Koma zinthu zawo zonse zimene anali kuchita zinali zowawonongetsa ndipo anazichitadi mofulumira.+