Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 22:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kenako mfumuyo inalamula wansembe Hilikiya, Ahikamu+ mwana wa Safani, Akibori mwana wa Mikaya, Safani mlembi, ndi Asaya+ mtumiki wa mfumu, kuti:

  • 2 Mbiri 34:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Kenako mfumuyo inalamula Hilikiya,+ Ahikamu+ mwana wa Safani, Abidoni mwana wa Mika, Safani+ mlembi,+ ndi Asaya+ mtumiki wa mfumu, kuti:

  • Yeremiya 39:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Iwo anatuma anthuwo kuti akatenge Yeremiya m’Bwalo la Alonda+ ndi kumupereka kwa Gedaliya+ mwana wa Ahikamu,+ mwana wa Safani,+ kuti apite naye kunyumba kwake, kuti Yeremiyayo akakhale pakati pa anthu akwawo.

  • Yeremiya 40:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Koma Yeremiya anali asanaganize zobwerera pamene Nebuzaradani anamuuza kuti: “Bwerera kwa Gedaliya,+ mwana wa Ahikamu,+ mwana wa Safani,+ amene mfumu ya Babulo yamuika kukhala wolamulira mizinda ya Yuda. Ukakhale naye pakati pa anthu ako ndipo ukapite kulikonse kumene ungakonde kupita.”+

      Pamenepo mkulu wa asilikali olondera mfumu anamupatsa chakudya chapaulendo ndi mphatso ndipo anamulola kupita.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena