Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 85:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Mwakhululukira anthu anu zolakwa zawo.+

      Mwaphimba machimo awo onse.+ [Seʹlah.]

  • Yesaya 40:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Mulankhuleni Yerusalemu momufika pamtima.+ Muuzeni mofuula kuti ntchito yake yogwira mokakamizidwa yatha,+ ndiponso kuti zolakwa zake zalipiridwa.+ Pakuti kuchokera m’dzanja la Yehova, iye walandira malipiro okwanira a machimo ake onse.”+

  • Yeremiya 31:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 “Munthu sadzaphunzitsanso mnzake kapena m’bale wake+ kuti, ‘Mum’dziwe Yehova!’+ pakuti aliyense wa iwo adzandidziwa, kuyambira wamng’ono mpaka wamkulu,”+ watero Yehova. “Ine ndidzawakhululukira zolakwa zawo ndipo machimo awo sindidzawakumbukiranso.”+

  • Zekariya 13:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 “Pa tsiku limenelo,+ kudzakumbidwa chitsime+ kuti a m’nyumba ya Davide ndi anthu okhala mu Yerusalemu adzayeretsedwe ku machimo+ ndi ku zinthu zawo zonyansa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena