2 Mbiri 30:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kuwonjezera apo, Hezekiya analankhula mokoma mtima+ kwa Alevi onse amene anali kutumikira Yehova mwanzeru.+ Anthuwo anachita phwando loikidwiratu kwa masiku 7.+ Anali kupereka nsembe zachiyanjano+ ndi kulapa+ kwa Yehova Mulungu wa makolo awo. Hoseya 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “‘Choncho ndidzalankhula naye ndi kumukhutiritsa kuti achoke ndi kupita kuchipululu,+ ndipo ndidzalankhula naye momufika pamtima.+
22 Kuwonjezera apo, Hezekiya analankhula mokoma mtima+ kwa Alevi onse amene anali kutumikira Yehova mwanzeru.+ Anthuwo anachita phwando loikidwiratu kwa masiku 7.+ Anali kupereka nsembe zachiyanjano+ ndi kulapa+ kwa Yehova Mulungu wa makolo awo.
14 “‘Choncho ndidzalankhula naye ndi kumukhutiritsa kuti achoke ndi kupita kuchipululu,+ ndipo ndidzalankhula naye momufika pamtima.+