Luka 20:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma nyengo ya zipatso itakwana anatumiza kapolo+ wake kwa alimiwo,+ kuti akamupatseko zina mwa zipatso za m’munda wa mpesawo.+ Komano alimiwo anamumenya ndi kumubweza chimanjamanja.+ 2 Akorinto 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndi atumiki a Khristu kapena? Ndikuyankha ngati wamisala, ineyo ndiye weniweni woposanso iwowo:+ m’ntchito zovuta mowirikiza koposa,+ m’ndende osachita kunena,+ kumenyedwa kosawerengeka, kutsala pang’ono kufa kawirikawiri.+ Aheberi 11:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ena analandira mayesero awo mwa kutonzedwa ndi kukwapulidwa, komanso kuposa pamenepo, mwa maunyolo+ ndi ndende.+
10 Koma nyengo ya zipatso itakwana anatumiza kapolo+ wake kwa alimiwo,+ kuti akamupatseko zina mwa zipatso za m’munda wa mpesawo.+ Komano alimiwo anamumenya ndi kumubweza chimanjamanja.+
23 Ndi atumiki a Khristu kapena? Ndikuyankha ngati wamisala, ineyo ndiye weniweni woposanso iwowo:+ m’ntchito zovuta mowirikiza koposa,+ m’ndende osachita kunena,+ kumenyedwa kosawerengeka, kutsala pang’ono kufa kawirikawiri.+
36 Ena analandira mayesero awo mwa kutonzedwa ndi kukwapulidwa, komanso kuposa pamenepo, mwa maunyolo+ ndi ndende.+