Yobu 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Satana+ anamuyankha Yehova kuti: “Khungu kusinthanitsa ndi khungu. Munthu angalolere kupereka chilichonse chimene ali nacho kuti apulumutse moyo wake.+ Miyambo 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Moyo wa munthu udzawomboledwa ndi chuma chake,+ koma munthu wosauka sadzudzulidwa.+ Mlaliki 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti nzeru zimateteza+ monga mmene ndalama zimatetezera,+ koma ubwino wa kudziwa zinthu ndi wakuti nzeru zimasunga moyo wa eni nzeruzo.+
4 Koma Satana+ anamuyankha Yehova kuti: “Khungu kusinthanitsa ndi khungu. Munthu angalolere kupereka chilichonse chimene ali nacho kuti apulumutse moyo wake.+
12 Pakuti nzeru zimateteza+ monga mmene ndalama zimatetezera,+ koma ubwino wa kudziwa zinthu ndi wakuti nzeru zimasunga moyo wa eni nzeruzo.+