Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Dziko lanu ndidzalisandutsa bwinja,+ ndipo adani anu amene adzakhala m’dzikolo adzaliyang’anitsitsa modabwa.+

  • Yeremiya 10:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Tamvetserani nkhani imene yamveka! Kugunda kwakukulu kukumveka kuchokera kudziko la kumpoto,+ ndipo kudzasandutsa mizinda ya Yuda kukhala mabwinja, malo obisalamo mimbulu.+

  • Yeremiya 12:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Cholowa changacho achisandutsa bwinja+ moti chafota ndipo chawonongeka.+ Dziko lonse lakhala bwinja ndipo palibe aliyense amene zikumukhudza.+

  • Ezekieli 11:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Nditangomaliza kulosera, Pelatiya mwana wa Benaya anamwalira.+ Choncho ine ndinagwada n’kuwerama mpaka nkhope yanga pansi, n’kufuula+ kuti: “Kalanga ine, inu Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa!+ Kodi mukufuna kufafaniziratu Aisiraeli otsalawa?”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena