Salimo 37:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzaonetsa poyera kulungama kwako kuti kuunike ngati kuwala,+Adzaonetsa poyera chilungamo chako kuti chiwale ngati usana.+ Mika 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mkwiyo waukulu wa Yehova ndiupirira chifukwa ndamuchimwira.+ Ndiupirirabe kufikira ataweruza mlandu wanga mondikomera ndi kundichitira chilungamo.+ Iye adzandipititsa pamalo owala ndipo ndidzaona kulungama kwake.+
6 Iye adzaonetsa poyera kulungama kwako kuti kuunike ngati kuwala,+Adzaonetsa poyera chilungamo chako kuti chiwale ngati usana.+
9 Mkwiyo waukulu wa Yehova ndiupirira chifukwa ndamuchimwira.+ Ndiupirirabe kufikira ataweruza mlandu wanga mondikomera ndi kundichitira chilungamo.+ Iye adzandipititsa pamalo owala ndipo ndidzaona kulungama kwake.+