Ekisodo 32:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndileke tsopano kuti mkwiyo wanga uwayakire ndipo ndiwafafanize,+ koma iwe ndikupange kukhala mtundu waukulu.”+ Yeremiya 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Tsopano iwe, usawapempherere anthu awa, ndipo usawalirire kwa ine mochonderera. Usawaperekere pemphero,+ chifukwa ine sindidzamvetsera pamene iwo akundiitana chifukwa cha tsoka limene lawagwera.+ Yeremiya 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova anapitiriza kundiuza kuti: “Usapempherere anthu awa kuti zinthu ziwayendere bwino.+
10 Ndileke tsopano kuti mkwiyo wanga uwayakire ndipo ndiwafafanize,+ koma iwe ndikupange kukhala mtundu waukulu.”+
14 “Tsopano iwe, usawapempherere anthu awa, ndipo usawalirire kwa ine mochonderera. Usawaperekere pemphero,+ chifukwa ine sindidzamvetsera pamene iwo akundiitana chifukwa cha tsoka limene lawagwera.+