Yeremiya 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Tsopano iwe usawapempherere anthu awa, kapena kuwalirira kwa ine mochonderera. Usawaperekere pemphero, kapena kuwapemphera mochonderera,+ chifukwa ine sindidzakumvetsera.+ Yeremiya 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Tsopano iwe, usawapempherere anthu awa, ndipo usawalirire kwa ine mochonderera. Usawaperekere pemphero,+ chifukwa ine sindidzamvetsera pamene iwo akundiitana chifukwa cha tsoka limene lawagwera.+
16 “Tsopano iwe usawapempherere anthu awa, kapena kuwalirira kwa ine mochonderera. Usawaperekere pemphero, kapena kuwapemphera mochonderera,+ chifukwa ine sindidzakumvetsera.+
14 “Tsopano iwe, usawapempherere anthu awa, ndipo usawalirire kwa ine mochonderera. Usawaperekere pemphero,+ chifukwa ine sindidzamvetsera pamene iwo akundiitana chifukwa cha tsoka limene lawagwera.+