Yobu 37:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Amuna inu mvetserani mwatcheru kugunda kwa mawu a Mulungu,+Ndi kubangula kochokera m’kamwa mwake. Yobu 38:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kodi ungafuulire mtamboKuti madzi ochuluka akukhuthukire?+ Yobu 38:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndani anaika nzeru+ m’mitambo,Kapena zinthu zochitika kuthambo, ndani anazipatsa kuzindikira?+ Salimo 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ali kumwamba, Yehova anayamba kugunda ngati mabingu,+Wam’mwambamwamba anayamba kutulutsa mawu ake,+Anatulutsanso matalala ndi makala onyeka a moto. Salimo 68:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Imbirani Iye wokwera kumwamba kwa kumwamba kwakale.+Tamverani! Iye akulankhula ndi mawu amphamvu.+
13 Ali kumwamba, Yehova anayamba kugunda ngati mabingu,+Wam’mwambamwamba anayamba kutulutsa mawu ake,+Anatulutsanso matalala ndi makala onyeka a moto.
33 Imbirani Iye wokwera kumwamba kwa kumwamba kwakale.+Tamverani! Iye akulankhula ndi mawu amphamvu.+