Salimo 78:60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 Pamapeto pake anasiya chihema chopatulika cha ku Silo,+Hema limene anali kukhalamo pakati pa anthu ochokera kufumbi.+ Hoseya 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Zoipa zawo zonse zinachitikira ku Giligala,+ ndipo ndinadana nawo kwambiri kumeneko.+ Chifukwa cha zochita zawo zoipa, ndidzawathamangitsa panyumba yanga.+ Sindidzapitiriza kuwakonda.+ Akalonga awo onse akuchita makani.+ Luka 13:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Tsopano tamverani! Mulungu wachoka ndi kukusiyirani nyumba* yanuyi.+ Ndithu ndikukuuzani, simudzandionanso kufikira pamene mudzanene kuti, ‘Wodalitsidwa iye wobwera m’dzina la Yehova!’”+
60 Pamapeto pake anasiya chihema chopatulika cha ku Silo,+Hema limene anali kukhalamo pakati pa anthu ochokera kufumbi.+
15 “Zoipa zawo zonse zinachitikira ku Giligala,+ ndipo ndinadana nawo kwambiri kumeneko.+ Chifukwa cha zochita zawo zoipa, ndidzawathamangitsa panyumba yanga.+ Sindidzapitiriza kuwakonda.+ Akalonga awo onse akuchita makani.+
35 Tsopano tamverani! Mulungu wachoka ndi kukusiyirani nyumba* yanuyi.+ Ndithu ndikukuuzani, simudzandionanso kufikira pamene mudzanene kuti, ‘Wodalitsidwa iye wobwera m’dzina la Yehova!’”+