Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 26:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Davideyo anawonjezera kuti: “N’chifukwa chiyani inu mbuyanga mukuthamangitsa ine mtumiki wanu?+ Ndachita chiyani ine, ndipo ndalakwa chiyani?+

  • Salimo 35:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Iwo andikumbira mbuna popanda chifukwa ndi kuikapo ukonde,+

      Akumba mbunazo kuti ndigweremo ngakhale kuti sindinalakwe.+

  • Salimo 69:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Anthu amene amadana nane popanda chifukwa achuluka kuposa tsitsi la m’mutu mwanga.+

      Amene akufuna kunditsitsira kuli chete, chifukwa chodana nane popanda chifukwa, achuluka kwambiri.+

      Ngakhale kuti sindine wakuba, anandikakamiza kubweza zinthu zimene zinabedwa.

  • Salimo 109:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Andizungulira ndi mawu achidani,+

      Ndipo akulimbana nane popanda chifukwa.+

  • Salimo 119:161
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 161 Akalonga andizunza popanda chifukwa,+

      Koma mtima wanga umaopa mawu anu.+

  • Yeremiya 37:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Pamenepo Yeremiya anafunsa Mfumu Zedekiya kuti: “Kodi ineyo ndakulakwirani chiyani pamodzi ndi atumiki anu ndiponso anthu onse,+ kuti munditsekere m’ndende?

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena