Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 25:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Chifukwa cha dzina lanu, inu Yehova,+

      Mundikhululukire cholakwa changa ngakhale kuti n’chachikulu.+

  • Salimo 79:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Tithandizeni inu Mulungu wa chipulumutso chathu,+

      Kuti dzina lanu lilemekezedwe.+

      Tipulumutseni ndi kutikhululukira* machimo athu chifukwa cha dzina lanu.+

  • Yeremiya 14:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ngakhale kuti zolakwa zathu n’zoonekeratu, inu Yehova, chitanipo kanthu chifukwa cha dzina lanu,+ pakuti zochita zathu zosonyeza kusakhulupirika zachuluka+ ndipo takuchimwirani.+

  • Danieli 9:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Imvani, inu Yehova.+ Tikhululukireni, inu Yehova.+ Timvereni ndipo muchitepo kanthu,+ inu Yehova. Inu Mulungu wanga, chifukwa cha dzina lanu musazengereze,+ pakuti mzinda wanu ndi anthu anu amatchedwa ndi dzina lanu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena