Ezekieli 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako mzimu wa Yehova unafika pa ine,+ ndipo iye anandiuza kuti: “Unene kuti, ‘Yehova wanena kuti:+ “Inu anthu a nyumba ya Isiraeli, mwanena bwino, ndipo ine ndadziwa maganizo anu.+
5 Kenako mzimu wa Yehova unafika pa ine,+ ndipo iye anandiuza kuti: “Unene kuti, ‘Yehova wanena kuti:+ “Inu anthu a nyumba ya Isiraeli, mwanena bwino, ndipo ine ndadziwa maganizo anu.+