Ezekieli 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nthambi za mtengowo zinakhala zolimba zoyenera kupangira ndodo zachifumu za olamulira.+ Patapita nthawi, mtengowo unatalika kwambiri kuposa mitengo ina, ndipo unali kuonekera patali chifukwa cha kutalika kwake ndi kuchuluka kwa masamba ake.+
11 Nthambi za mtengowo zinakhala zolimba zoyenera kupangira ndodo zachifumu za olamulira.+ Patapita nthawi, mtengowo unatalika kwambiri kuposa mitengo ina, ndipo unali kuonekera patali chifukwa cha kutalika kwake ndi kuchuluka kwa masamba ake.+