Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 106:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Iwo anayamba kusakanikirana ndi mitundu ina,+

      Ndi kuyamba kuphunzira zochita zawo.+

  • Yeremiya 2:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ndiyeno n’chifukwa chiyani ukufuna kuyenda m’njira ya ku Iguputo+ kuti ukamwe madzi a mumtsinje wa Sihori?+ N’chifukwa chiyani ukufuna kuyenda m’njira yopita kudziko la Asuri+ kuti ukamwe madzi a mumtsinje wa Firate?

  • Yeremiya 16:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pamenepo udzawayankhe kuti, ‘“N’chifukwa chakuti makolo anu anandisiya,”+ watero Yehova, “ndipo anapitirizabe kutsatira milungu ina, kuitumikira ndi kuigwadira.+ Koma ine anandisiya ndipo sanasunge malamulo anga.+

  • Yeremiya 22:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndipo adzanena kuti: “Anauchitira zimenezi chifukwa chakuti anthu a mumzindawu anasiya pangano la Yehova Mulungu wawo+ ndi kuyamba kulambira milungu ina ndi kuitumikira.”’+

  • Ezekieli 6:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Opulumuka anu akadzagwidwa n’kutengedwa kukakhala pakati pa mitundu ina ya anthu, ndithu adzandikumbukira.+ Adzakumbukira mmene ndinamvera kupweteka chifukwa cha mtima wawo wadama umene unawachititsa kundipandukira.+ Adzakumbukiranso mmene ndinamvera kupweteka chifukwa cha maso awo othamangira mafano awo onyansa pofuna kuchita nawo zadama.+ Iwo adzachita manyazi ochita kuonekera pankhope zawo, chifukwa cha zinthu zonse zoipa ndi zonyansa zimene anachita.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena