Yeremiya 39:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zitatero mfumu ya Babulo inapha+ ana aamuna a Zedekiya ku Ribila, Zedekiyayo akuona.+ Inaphanso akuluakulu onse a ku Yuda.+ Ezekieli 34:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Nkhosa zosochera ndidzazifunafuna,+ zomwazika ndidzazibweza. Yothyoka mwendo ndidzaimanga mwendo wothyokawo. Yodwala ndidzailimbitsa, koma yonenepa+ ndi yamphamvu ndidzaiwononga. Ndidzaipatsa chiweruzo monga chakudya chake.”+
6 Zitatero mfumu ya Babulo inapha+ ana aamuna a Zedekiya ku Ribila, Zedekiyayo akuona.+ Inaphanso akuluakulu onse a ku Yuda.+
16 “Nkhosa zosochera ndidzazifunafuna,+ zomwazika ndidzazibweza. Yothyoka mwendo ndidzaimanga mwendo wothyokawo. Yodwala ndidzailimbitsa, koma yonenepa+ ndi yamphamvu ndidzaiwononga. Ndidzaipatsa chiweruzo monga chakudya chake.”+