Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 15:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pamenepo mafumu a ku Edomu adzasokonezeka.

      Ndipo olamulira amphamvu a ku Mowabu adzanjenjemera ndi mantha.+

      Ndithu, anthu onse okhala mu Kanani adzataya mtima.+

  • Ezekieli 27:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Anthu onse okhala m’zilumba+ adzakuyang’anitsitsa modabwa ndipo mafumu awo adzanjenjemera chifukwa cha mantha.+ Nkhope zawo zonse zidzaoneka zankhawa.+

  • Ezekieli 32:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndidzachititsa mantha anthu ambiri a mitundu ina chifukwa cha iwe.+ Ndikadzawaloza ndi lupanga langa kumaso,+ mafumu awo adzanjenjemera ndi mantha. Kuyambira pa tsiku limene udzaphedwe, aliyense wa iwo azidzanjenjemera nthawi zonse chifukwa choopa kufa.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena