Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 3:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 (Asidoni anali kutcha phiri la Herimoni kuti Sirioni,+ pamene Aamori anali kulitcha kuti Seniri.)+

  • 1 Mbiri 5:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ana a hafu ya fuko la Manase+ anakhala m’dera loyambira ku Basana+ mpaka ku Baala-herimoni,+ ku Seniri,+ ndi kuphiri la Herimoni,+ ndipo iwo anachulukana kwambiri.

  • Nyimbo ya Solomo 4:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Tiye tichokere limodzi ku Lebanoni, iwe mkwatibwi wanga,+ tiye tichoke ku Lebanoni.+ Utsetsereke kuchokera pamwamba pa phiri la Amana, kuchokera pamwamba pa phiri la Seniri,+ ngakhalenso pamwamba pa phiri la Herimoni.+ Utsetsereke kuchokera m’mapanga a mikango, ndiponso kuchokera kumapiri a akambuku.*

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena