6 Onsewo adzasiyidwa kuti mbalame za m’mapiri zodya nyama, ndi nyama zakutchire za padziko lapansi,+ ziwadye. Mbalame zodya nyamazo zidzakhala zikuwadya chilimwe chonse, ndipo nyama zonse zakutchire za padziko lapansi zidzakhala zikuwadya m’nyengo yonse yokolola.+