Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 10:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Tsopano akerubi aja anatambasula mapiko awo n’kunyamuka kuchoka pansi+ ine ndikuona. Atanyamuka, mawilo aja anali pambali pawo. Kenako iwo anakaima pakhomo la kum’mawa la chipata cha nyumba ya Yehova, ndipo ulemerero wa Mulungu wa Isiraeli unali pamwamba pawo.

  • Ezekieli 40:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Kenako anafika pachipata chimene chinayang’ana kum’mawa+ ndipo anakwera pamasitepe ake. Pamenepo iye anayamba kuyeza malo apafupi ndi khomo la kanyumba ka pachipatako+ ndipo anapeza kuti malowo anali bango limodzi m’lifupi. Malo apafupi ndi khomo la mbali ina ya kanyumbako analinso bango limodzi m’lifupi mwake.

  • Ezekieli 42:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Choncho anamaliza kuyeza nyumba yamkati, ndipo ananditulutsa kudzera pachipata chimene chinayang’ana kum’mawa.+ Kenako anayeza malo onsewo.

  • Ezekieli 44:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 Kenako munthu uja ananditengeranso kuchipata chakunja cha malo opatulika, chimene chinayang’ana kum’mawa,+ ndipo tinapeza kuti chinali chotseka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena