Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 1:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kenako Yehova anandifunsanso kachiwiri kuti: “Ukuona chiyani?”

      Ine ndinayankha kuti: “Ndikuona mphika wakukamwa kwakukulu umene uli pamoto, ndipo motowo aupemerera kuti uyake kwambiri. Mphikawo wafulatira kumpoto.”

  • Ezekieli 24:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Tsoka mzinda wokhetsa magazi,+ umene uli ngati mphika wakukamwa kwakukulu. Mphikawo uli ndi dzimbiri ndipo dzimbiri lakelo silikutha. Muchotsemo nthulizo imodziimodzi.+ Musachite maere pamphikawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena