Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 1:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Taonani! Mzinda wokhulupirika uja+ wasanduka hule.+ Unali wodzaza ndi chilungamo+ ndipo zachilungamo zinali kukhala mwa iye,+ koma tsopano muli zigawenga zopha anthu.+

  • Yeremiya 3:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Yehova anapitiriza kulankhula nane m’masiku a Mfumu Yosiya kuti:+ “‘Kodi waona zimene Isiraeli wosakhulupirikayu akuchita?+ Akupita kuphiri lililonse lalitali+ ndi pansi pa mtengo uliwonse waukulu wa masamba ambiri obiriwira+ kuti akachite uhule kumeneko.+

  • Hoseya 2:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 popeza mayi wawo wachita dama.+ Mayi amene anatenga pakati kuti awabereke wachita zinthu zochititsa manyazi+ ndipo wanena kuti, ‘Ndikufuna kutsatira amene anali kundikonda kwambiri+ ndiponso amene anali kundipatsa chakudya, madzi, zovala za ubweya wa nkhosa, nsalu, mafuta ndi zakumwa.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena