Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Zekariya 5:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndiyeno anandiuza kuti: “Ili ndi temberero limene likubwera padziko lonse lapansi,+ chifukwa aliyense amene akuba+ sakulandira chilango, monga mmene temberero limene lalembedwa kumbali imodzi ya mpukutuwo likunenera. Komanso aliyense amene akulumbira mwachinyengo+ sakulandira chilango, monga mmene temberero limene lalembedwa kumbali inayo ya mpukutuwo likunenera.+

  • Chivumbulutso 5:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Kenako, ndinaona mpukutu wolembedwa mkati ndi kunja komwe,+ uli m’dzanja lamanja la Iye wokhala pampando wachifumu.+ Unali womatidwa+ mwamphamvu ndi zidindo 7 zomatira.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena