Numeri 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Andanda kukafika kutali ngati zigwa,*+Ngati minda m’mphepete mwa mtsinje.+Ngati mitengo ya aloye imene Yehova anabzala,Ngati mikungudza m’mbali mwa madzi.+ Deuteronomo 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti Yehova Mulungu wanu akukulowetsani m’dziko labwino,+ dziko la zigwa* za madzi,+ akasupe ndi madzi ochuluka otuluka m’zigwa ndi m’madera a mapiri,
6 Andanda kukafika kutali ngati zigwa,*+Ngati minda m’mphepete mwa mtsinje.+Ngati mitengo ya aloye imene Yehova anabzala,Ngati mikungudza m’mbali mwa madzi.+
7 Pakuti Yehova Mulungu wanu akukulowetsani m’dziko labwino,+ dziko la zigwa* za madzi,+ akasupe ndi madzi ochuluka otuluka m’zigwa ndi m’madera a mapiri,