Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 8:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Mfumuyo idzakula mphamvu koma osati mwa iyo yokha.+ Idzawononga zinthu zambiri+ ndipo chilichonse chimene izidzachita chidzaiyendera bwino. Idzawononga anthu amphamvu ndi anthu oyera.+

  • Danieli 12:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Pamenepo ndinamva mwamuna wovala nsalu uja, amene anaimirira pamwamba pa madzi a mumtsinje akuyankha. Poyankhapo, anakweza m’mwamba dzanja lake lamanja ndi lamanzere ndi kulumbira+ pa Iye amene adzakhala ndi moyo mpaka kalekale,+ ndipo anati: “Padzapita nthawi imodzi yoikidwiratu, nthawi ziwiri zoikidwiratu, ndi hafu ya nthawi yoikidwiratu.+ Ndipo akadzangomaliza kuphwanyaphwanya+ mphamvu za anthu oyera, zinthu zonsezi zidzafika pamapeto.”

  • Chivumbulutso 11:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Zikamaliza kuchitira umboni wawo, chilombo chotuluka muphompho+ chidzachita nazo nkhondo, ndipo chidzazigonjetsa ndi kuzipha.+

  • Chivumbulutso 13:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Chinaloledwa+ kuchita nkhondo ndi oyerawo ndi kuwagonjetsa.+ Chinapatsidwanso ulamuliro pa anthu a fuko lililonse, mtundu uliwonse, chinenero chilichonse ndi dziko lililonse.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena