Danieli 2:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 “Pambuyo panu padzabwera ufumu wina+ wotsikirapo kwa inu.+ Kenako padzabweranso ufumu wina wachitatu, wamkuwa, umene udzalamulira dziko lonse lapansi.+ Danieli 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zilombo zinayi zikuluzikulu+ zinali kutuluka m’nyanjayo,+ ndipo chilichonse chinali chosiyana ndi chinzake.+ Danieli 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mbuzi yamphongo yaubweya wambiri ikuimira mfumu ya Girisi,+ ndipo nyanga yaikulu imene inali pakati pa maso ake ikuimira mfumu yoyamba.+
39 “Pambuyo panu padzabwera ufumu wina+ wotsikirapo kwa inu.+ Kenako padzabweranso ufumu wina wachitatu, wamkuwa, umene udzalamulira dziko lonse lapansi.+
3 Zilombo zinayi zikuluzikulu+ zinali kutuluka m’nyanjayo,+ ndipo chilichonse chinali chosiyana ndi chinzake.+
21 Mbuzi yamphongo yaubweya wambiri ikuimira mfumu ya Girisi,+ ndipo nyanga yaikulu imene inali pakati pa maso ake ikuimira mfumu yoyamba.+