Salimo 50:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa tsiku la nsautso undiitane.+Ine ndidzakulanditsa, ndipo iwe udzandilemekeza.”+ Salimo 145:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ntchito zanu zonse zidzakutamandani, inu Yehova,+Ndipo okhulupirika anu adzakutamandani.+