Danieli 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Choncho iye* adzabwerera kudziko lakwawo ali ndi katundu wochuluka ndipo adzakhala ndi mtima wofuna kuukira pangano lopatulika+ moti adzakwaniritsa+ zolinga zake n’kubwerera kwawo.
28 “Choncho iye* adzabwerera kudziko lakwawo ali ndi katundu wochuluka ndipo adzakhala ndi mtima wofuna kuukira pangano lopatulika+ moti adzakwaniritsa+ zolinga zake n’kubwerera kwawo.