Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 111:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Chiyambi cha nzeru ndicho kuopa Yehova.+

      ש [Sin]

      Onse otsatira malamulo a Mulungu ndi ozindikira.+

      ת [Taw]

      Iye ayenera kutamandidwa mpaka muyaya.+

  • Miyambo 3:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ukachita zimenezi, Mulungu ndi anthu adzakukomera mtima ndipo adzakuona kuti ndiwe wozindikira.+

  • Danieli 11:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Anthu ozindikira+ pakati pa anthuwo adzathandiza anthu ambiri kumvetsa zinthu.+ Iwo adzapunthwa kwa kanthawi ndi lupanga ndi malawi a moto. Adzapunthwanso mwa kutengedwa ukapolo ndi kuwonongedwa kwa zinthu zawo.+

  • Danieli 12:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Anthu ozindikira adzawala ngati kuwala kwa kuthambo.+ Ndipo amene akuthandiza anthu ambiri kukhala olungama+ adzawala ngati nyenyezi mpaka kalekale, inde, kwamuyaya.

  • 1 Yohane 5:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Tikudziwa kuti Mwana wa Mulungu anabwera,+ ndipo anatipatsa nzeru+ kuti timudziwe woonayo.+ Ndipo ife ndife ogwirizana+ ndi woonayo, kudzera mwa Mwana wake Yesu Khristu. Iyeyo ndiye Mulungu woona+ ndiponso wopereka moyo wosatha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena