Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 26:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 “Anthu anu amene anafa adzakhalanso ndi moyo.+ Anthu anga amene anafa adzadzuka ndi kuimirira.+ Inu anthu okhala m’fumbi, dzukani, fuulani mokondwera!+ Pakuti mame anu+ ali ngati mame a maluwa,+ ndipo dziko lapansi lidzabereka anthu amene anafa.+

  • Danieli 12:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Anthu ambiri amene agona munthaka adzauka.+ Ena adzalandira moyo wosatha+ koma ena adzalandira chitonzo ndipo adzadedwa mpaka kalekale.+

  • Mateyu 22:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Kunena za kuuka kwa akufa, kodi simunawerenge zimene Mulungu ananena kwa inu kuti,+

  • Yohane 5:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Musadabwe nazo zimenezi, chifukwa idzafika nthawi pamene onse ali m’manda achikumbutso+ adzamva mawu ake

  • Yohane 11:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Pamenepo Yesu anati: “Ine ndine kuuka ndi moyo.+ Aliyense wokhulupirira mwa ine, ngakhale amwalire, adzakhalanso ndi moyo.+

  • Chivumbulutso 20:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndiye ndinaona akufa, olemekezeka ndi onyozeka,+ ataimirira pamaso pa mpando wachifumuwo, ndipo mipukutu inafunyululidwa. Koma mpukutu wina unafunyululidwa, ndiwo mpukutu wa moyo.+ Ndipo akufa anaweruzidwa malinga ndi zolembedwa m’mipukutuyo, mogwirizana ndi ntchito zawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena