Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 10:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndipo dzombelo linayamba kufika m’dziko lonse la Iguputo ndi kutera m’madera onse a dzikolo.+ Linawasautsa kwambiri.+ Dzombe ngati limeneli linali lisanagwepo n’kale lonse ndipo sipadzagwanso lina ngati limeneli.

  • Ekisodo 13:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “Ndiyeno m’tsogolo, mwana wanu akadzakufunsani+ kuti, ‘Kodi zimenezi zikutanthauza chiyani?’ Mudzamuyankhe kuti, ‘Yehova anatitulutsa ndi mphamvu ya dzanja lake mu Iguputo,+ m’nyumba ya ukapolo.+

  • Deuteronomo 6:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 ndi kuwakhomereza mwa ana ako.+ Uzilankhula nawo za mawuwo ukakhala pansi m’nyumba mwako, poyenda pamsewu, pogona+ ndi podzuka.

  • Deuteronomo 29:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 “Pamenepo m’badwo wa m’tsogolo, ana anu amene adzabwera pambuyo panu, ndiponso mlendo amene adzachokera kudziko lakutali, akadzaona miliri ndi nthenda zimene Yehova wakantha nazo dzikolo,+ adzanena mawu.

  • Salimo 78:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Mbadwa zawo sitikuzibisira mawu ophiphiritsawa,+

      Ndipo tidzawasimba ngakhale ku mibadwo ya m’tsogolo.+

      Tidzasimba ntchito zotamandika za Yehova ndi mphamvu zake,+

      Komanso zinthu zodabwitsa zimene wachita.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena