Yesaya 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Dzikolo likudzandira ngati munthu woledzera. Likugwedezekera uku ndi uku ngati chisimba.+ Zolakwa za dzikolo n’zolemera+ ndipo lidzagwa nazo osadzukanso.+
20 Dzikolo likudzandira ngati munthu woledzera. Likugwedezekera uku ndi uku ngati chisimba.+ Zolakwa za dzikolo n’zolemera+ ndipo lidzagwa nazo osadzukanso.+