Maliko 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Andireya, Filipo, Batolomeyo, Mateyu, Tomasi, Yakobo mwana wa Alifeyo, Tadeyo, Simoni Kananiya,* Luka 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye anasankha Simoni, amenenso anam’patsa dzina lakuti Petulo,+ ndi m’bale wake Andireya. Anasankhanso Yakobo ndi Yohane,+ Filipo+ ndi Batolomeyo, Yohane 1:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Kenako Filipo anapeza Natanayeli+ n’kumuuza kuti: “Uja amene Mose analemba za iye m’Chilamulo+ komanso wotchulidwa m’Zolemba za aneneri,+ ife tam’peza. Iyeyu ndi Yesu, mwana wa Yosefe,+ wa ku Nazareti.”
14 Iye anasankha Simoni, amenenso anam’patsa dzina lakuti Petulo,+ ndi m’bale wake Andireya. Anasankhanso Yakobo ndi Yohane,+ Filipo+ ndi Batolomeyo,
45 Kenako Filipo anapeza Natanayeli+ n’kumuuza kuti: “Uja amene Mose analemba za iye m’Chilamulo+ komanso wotchulidwa m’Zolemba za aneneri,+ ife tam’peza. Iyeyu ndi Yesu, mwana wa Yosefe,+ wa ku Nazareti.”